21

Q.S As-Sajdah (32:21)

وَلَنُذِيْقَنَّهُمْ مِّنَ الْعَذَابِ الْاَدْنٰى دُوْنَ الْعَذَابِ الْاَكْبَرِ لَعَلَّهُمْ يَرْجِعُوْنَ

wa lanużīqannahum minal-‘ażābil-adnā dūnal-‘ażābil-akbari la‘allahum yarji‘ūn(a).

Ndipo ndithu tidzawapatsa chilango chapafupi (padziko lapansi) chisanafike chilango chachikulu (cha pambuyo pa imfa), kuti abwerere (kunjira yowongoka).