41
Q.S Ali Imran (3:41)
قَالَ رَبِّ اجْعَلْ لِّيْٓ اٰيَةً ۗ قَالَ اٰيَتُكَ اَلَّا تُكَلِّمَ النَّاسَ ثَلٰثَةَ اَيَّامٍ اِلَّا رَمْزًا ۗ وَاذْكُرْ رَّبَّكَ كَثِيْرًا وَّسَبِّحْ بِالْعَشِيِّ وَالْاِبْكَارِ ࣖ
qāla rabbij‘al lī āyah(tan), qāla āyatuka allā tukalliman-nāsa ṡalāṡata ayyāmin illā ramzā(n), ważkur rabbaka kaṡīraw wa sabbiḥ bil-‘asyiyyi wal-ibkār(i).
Iye (Zakariya) anati, “O Ambuye wanga, ndipatseni chizindikiro.” Allah anati, “Chizindikiro kwa inu ndi chakuti simulankhula ndi anthu kwa masiku atatu, kupatulapo zizindikiro. Ndipo tchulani (dzina) la Ambuye wanu kwambiri, ndipo mlemekezeni (m’tamandeni) madzulo ndi m’mawa.”