40
Q.S Ali Imran (3:40)
قَالَ رَبِّ اَنّٰى يَكُوْنُ لِيْ غُلٰمٌ وَّقَدْ بَلَغَنِيَ الْكِبَرُ وَامْرَاَتِيْ عَاقِرٌ ۗ قَالَ كَذٰلِكَ اللّٰهُ يَفْعَلُ مَا يَشَاۤءُ
qāla rabbi annā yakūnu lī gulāmuw wa qad balaganīyal-kibaru wamra'atī ‘āqir(un), qāla każālikallāhu yaf‘alu mā yasyā'(u).
Iye (Zakariya) anati, "O Ambuye wanga, ndingakhale bwanji ndi ana pamene ndili wokalamba chonchi ndipo mkazi wanga ndi wosabereka?" Iye (Allah) anati, "Motero, Mulungu amachita zimene akufuna."