187

Q.S Ali Imran (3:187)

وَاِذْ اَخَذَ اللّٰهُ مِيْثَاقَ الَّذِيْنَ اُوْتُوا الْكِتٰبَ لَتُبَيِّنُنَّهٗ لِلنَّاسِ وَلَا تَكْتُمُوْنَهٗۖ فَنَبَذُوْهُ وَرَاۤءَ ظُهُوْرِهِمْ وَاشْتَرَوْا بِهٖ ثَمَنًا قَلِيْلًا ۗ فَبِئْسَ مَا يَشْتَرُوْنَ

wa iż akhażallāhu mīṡāqal-lażīna ūtul-kitāba latubayyinunnahū lin-nāsi wa lā taktumūnah(ū), fa nabażūhu warā'a ẓuhūrihim wasytarau bihī ṡamanan qalīlā(n), fa bi'sa mā yasytarūn(a).

Ndipo (kumbukirani), pamene Allah adatenga lonjezo kwa iwo omwe adapatsidwa Buku (lomwe ndi lakuti), "Muyenera kulifotokozera anthu moona mtima (zomwe zili m'Buku), ndipo musalibise," kenako adaliponya kumbuyo kwawo ndikuligulitsa pamtengo wotsika. Choncho umenewo ndi mtundu woipa kwambiri wa kugula ndi kugulitsa womwe amachita.