186

Q.S Ali Imran (3:186)

۞ لَتُبْلَوُنَّ فِيْٓ اَمْوَالِكُمْ وَاَنْفُسِكُمْۗ وَلَتَسْمَعُنَّ مِنَ الَّذِيْنَ اُوْتُوا الْكِتٰبَ مِنْ قَبْلِكُمْ وَمِنَ الَّذِيْنَ اَشْرَكُوْٓا اَذًى كَثِيْرًا ۗ وَاِنْ تَصْبِرُوْا وَتَتَّقُوْا فَاِنَّ ذٰلِكَ مِنْ عَزْمِ الْاُمُوْرِ

latublawunna fī amwālikum wa anfusikum, wa latasma‘unna minal-lażīna ūtul-kitāba min qablikum wa minal-lażīna asyrakū ażan kaṡīrā(n), wa in taṣbirū wa tattaqū fa inna żālika min ‘azmil-umūr(i).

Ndithudi mudzayesedwa ndi chuma chanu ndi inu nokha. Ndipo ndithudi mudzamva zinthu zambiri zopweteka kwambiri kuchokera kwa omwe adapatsidwa Buku patsogolo panu ndi ochokera kwa opembedza mafano. Ngati muli oleza mtima komanso opembedza, ndiye kuti zinthu zimenezo ndi zinthu zomwe ziyenera kuyikidwa patsogolo.