173

Q.S Ali Imran (3:173)

اَلَّذِيْنَ قَالَ لَهُمُ النَّاسُ اِنَّ النَّاسَ قَدْ جَمَعُوْا لَكُمْ فَاخْشَوْهُمْ فَزَادَهُمْ اِيْمَانًاۖ وَّقَالُوْا حَسْبُنَا اللّٰهُ وَنِعْمَ الْوَكِيْلُ

al-lażīna qāla lahumun-nāsu innan-nāsa qad jama‘ū lakum fakhsyauhum fa zādahum īmānā(n), wa qālū ḥasbunallāhu wa ni‘mal-wakīl(u).

(Ndiye) amene (omvera Allah ndi Mtumiki) amene, anthu akawauza kuti, “Anthu (a Quraysh) asonkhanitsa gulu lankhondo motsutsana nanu, choncho opani,” zimawonjezera chikhulupiriro chawo ndipo amati, “Mulungu akutikwanira, ndipo Iye ndiye mtetezi wabwino kwambiri.”