172
Q.S Ali Imran (3:172)
اَلَّذِيْنَ اسْتَجَابُوْا لِلّٰهِ وَالرَّسُوْلِ مِنْۢ بَعْدِ مَآ اَصَابَهُمُ الْقَرْحُ ۖ لِلَّذِيْنَ اَحْسَنُوْا مِنْهُمْ وَاتَّقَوْا اَجْرٌ عَظِيْمٌۚ
al-lażīnastajābū lillāhi war-rasūli mim ba‘di mā aṣābahumul-qarḥ(u), lil-lażīna aḥsanū minhum wattaqau ajrun ‘aẓīm(un).
(Ndiye) amene amamvera Mulungu ndi Mtumiki pambuyo poti avulala (pa Nkhondo ya Uhud). Amene amachita zabwino ndi opembedza pakati pawo adzapeza mphotho yayikulu.