166

Q.S Ali Imran (3:166)

وَمَآ اَصَابَكُمْ يَوْمَ الْتَقَى الْجَمْعٰنِ فَبِاِذْنِ اللّٰهِ وَلِيَعْلَمَ الْمُؤْمِنِيْنَۙ

wa mā aṣābakum yaumal-taqal-jam‘āni fa bi'iżnillāhi wa liya‘lamal-mu'minīn(a).

Ndipo chimene chidakugwerani pamene magulu awiriwa adakumana chinali mwa chilolezo cha Mulungu, ndi kuti Mulungu awayese okhulupirira enieni.