165
Q.S Ali Imran (3:165)
اَوَلَمَّآ اَصَابَتْكُمْ مُّصِيْبَةٌ قَدْ اَصَبْتُمْ مِّثْلَيْهَاۙ قُلْتُمْ اَنّٰى هٰذَا ۗ قُلْ هُوَ مِنْ عِنْدِ اَنْفُسِكُمْ ۗ اِنَّ اللّٰهَ عَلٰى كُلِّ شَيْءٍ قَدِيْرٌ
awa lammā aṣābatkum muṣībatun qad aṣabtum miṡlaihā, qultum annā hāżā, qul huwa min ‘indi anfusikum, innallāha ‘alā kulli syai'in qadīr(un).
Ndipo bwanji mukudabwa pamene tsoka (kugonjetsedwa ku Uhud) lakugwerani, pamene mwawachitira adani anu tsoka lalikulu kawiri kuposa limenelo ku Badr? Mumati, “Kodi (kugonjetsedwa) kumeneku kwachokera kuti?” Nenani, “Kwachokera kwa inu nokha.” Ndithudi, Mulungu ali ndi mphamvu pa chilichonse.