98
Q.S Yona (10:98)
فَلَوْلَا كَانَتْ قَرْيَةٌ اٰمَنَتْ فَنَفَعَهَآ اِيْمَانُهَآ اِلَّا قَوْمَ يُوْنُسَۗ لَمَّآ اٰمَنُوْا كَشَفْنَا عَنْهُمْ عَذَابَ الْخِزْيِ فِى الْحَيٰوةِ الدُّنْيَا وَمَتَّعْنٰهُمْ اِلٰى حِيْنٍ
falau lā kānat qaryatun āmanat fa nafa‘ahā īmānuhā illā qauma yūnus(a), lammā āmanū kasyafnā ‘anhum ‘ażābal-khizyi fil-ḥayātid-dun-yā wa matta‘nāhum ilā ḥīn(in).
Nanga bwanji palibe (wokhala) m'dziko amene akhulupirira, ndipo chikhulupiriro chake chili chopindulitsa kwa iye kupatula anthu a Yona? Pamene iwo (anthu a Yunus) adakhulupirira, tidawachotsera chilango chonyoza cha moyo wapadziko lapansi, ndipo tidawapatsa chisangalalo kwa nthawi inayake.