95
Q.S Yona (10:95)

وَلَا تَكُوْنَنَّ مِنَ الَّذِيْنَ كَذَّبُوْا بِاٰيٰتِ اللّٰهِ فَتَكُوْنَ مِنَ الْخٰسِرِيْنَ

wa lā takūnanna minal-lażīna każżabū bi'āyātillāhi fa takūna minal-khāsirīn(a).

Ndipo usakhale m'gulu la anthu otsutsa ma Aya a Mulungu, kapena udzakhala m'gulu la anthu omwe adzataya.