133
Q.S Al-A'raf (7:133)
فَاَرْسَلْنَا عَلَيْهِمُ الطُّوْفَانَ وَالْجَرَادَ وَالْقُمَّلَ وَالضَّفَادِعَ وَالدَّمَ اٰيٰتٍ مُّفَصَّلٰتٍۗ فَاسْتَكْبَرُوْا وَكَانُوْا قَوْمًا مُّجْرِمِيْنَ
fa arsalnā ‘alaihimuṭ-ṭūfāna wal-jarāda wal-qummala waḍ-ḍafādi‘a wad-dama āyātim mufaṣṣalāt(in), fastakbarū wa kānū qaumam mujrimīn(a).
Choncho tidawatumizira mphepo yamkuntho, dzombe, nsabwe, achule ndi magazi (madzi akumwa osanduka magazi) ngati zizindikiro zomveka bwino, koma adakhalabe odzikuza ndipo anali anthu ochimwa.
7
Q.S Al-Qamar (54:7)
خُشَّعًا اَبْصَارُهُمْ يَخْرُجُوْنَ مِنَ الْاَجْدَاثِ كَاَنَّهُمْ جَرَادٌ مُّنْتَشِرٌۙ
khusysya‘an abṣāruhum yakhrujūna minal-ajdāṡi ka'annahum jarādum muntasyir(un).
maso awo anali odzaza ndi chisoni, pamene anatuluka m'manda, ngati kuti anali ziwala zouluka,