فَانْطَلَقَا ۗحَتّٰٓى اِذَا لَقِيَا غُلٰمًا فَقَتَلَهٗ ۙقَالَ اَقَتَلْتَ نَفْسًا زَكِيَّةً؈ۢبِغَيْرِ نَفْسٍۗ لَقَدْ جِئْتَ شَيْـًٔا نُّكْرًا ۔
fanṭalaqā, ḥattā iżā laqiyā gulāman fa qatalah(ū), qāla aqatalta nafsan zakiyyatam bigairi nafs(in), laqad ji'ta syai'an nukrā(n).
Choncho onse awiri anayenda; mpaka awiriwa atakumana ndi mnyamata, anamupha. Iye (Mose) anati, "Bwanji mukupha munthu woyera, osati chifukwa chakuti wapha munthu wina? Ndithudi, mwachita chinthu choipa kwambiri."
وَاَمَّا الْغُلٰمُ فَكَانَ اَبَوَاهُ مُؤْمِنَيْنِ فَخَشِيْنَآ اَنْ يُّرْهِقَهُمَا طُغْيَانًا وَّكُفْرًا ۚ
wa ammal-gulāmu fa kāna abawāhu mu'minaini fa khasyīnā ay yurhiqahumā ṭugyānaw wa kufrā(n).
Ndipo za mnyamatayo (wosakhulupirira), makolo ake onse anali okhulupirira, ndipo tinkaopa kuti angakakamize makolo ake kusokera ndi kusakhulupirira.