73

Q.S Al-Anfal (8:73)

وَالَّذِيْنَ كَفَرُوْا بَعْضُهُمْ اَوْلِيَاۤءُ بَعْضٍۗ اِلَّا تَفْعَلُوْهُ تَكُنْ فِتْنَةٌ فِى الْاَرْضِ وَفَسَادٌ كَبِيْرٌۗ

wal-lażīna kafarū ba‘ḍuhum auliyā'u ba‘ḍ(in), illā taf‘alūhu takun fitnatun fil-arḍi wa fasādun kabīr(un).

Ndipo amene sakhulupirira, ena mwa iwo amateteza ena. Ngati simuchita zomwe Allah walamula (kutetezana wina ndi mnzake), padzakhala chisokonezo padziko lapansi ndi kuwonongeka kwakukulu.