7
Q.S Al-Anfal (8:7)
وَاِذْ يَعِدُكُمُ اللّٰهُ اِحْدَى الطَّاۤىِٕفَتَيْنِ اَنَّهَا لَكُمْ وَتَوَدُّوْنَ اَنَّ غَيْرَ ذَاتِ الشَّوْكَةِ تَكُوْنُ لَكُمْ وَيُرِيْدُ اللّٰهُ اَنْ يُّحِقَّ الْحَقَّ بِكَلِمٰتِهٖ وَيَقْطَعَ دَابِرَ الْكٰفِرِيْنَۙ
wa iż ya‘idukumullāhu iḥdaṭ-ṭā'ifataini annahā lakum wa tawaddūna anna gaira żātisy-syaukati takūnu lakum wa yurīdullāhu ay yuḥiqqal-ḥaqqa bikalimātihī wa yaqṭa‘a dābiral-kāfirīn(a).
Ndipo (kumbukirani) pamene Mulungu anakulonjezani kuti gulu limodzi mwa magulu awiri (munakumana nawo) lidzakhala lanu, pomwe inu munafuna kuti gulu lopanda zida likhale lanu, koma Mulungu akufuna kutsimikizira choonadi ndi zizindikiro zake ndi kuwawononga osakhulupirira m'mizu yawo.