67

Q.S Al-Anfal (8:67)

مَاكَانَ لِنَبِيٍّ اَنْ يَّكُوْنَ لَهٗٓ اَسْرٰى حَتّٰى يُثْخِنَ فِى الْاَرْضِۗ تُرِيْدُوْنَ عَرَضَ الدُّنْيَاۖ وَاللّٰهُ يُرِيْدُ الْاٰخِرَةَۗ وَاللّٰهُ عَزِيْزٌحَكِيْمٌ

mā kāna linabiyyin ay yakūna lahū asrā ḥattā yuṡkhina fil-arḍ(i), turīdūna ‘araḍad-dun-yā, wallāhu yurīdul-ākhirah(ta), wallāhu ‘azīzun ḥakīm(un).

Sizingakhale zoyenera kuti mneneri akhale ndi akaidi asanalemetse adani ake padziko lapansi. Mukufuna zinthu zapadziko lapansi pomwe Allah akufuna (mphoto) za moyo wa pambuyo pa imfa (kwa inu). Allah ndi wamphamvu zonse, wanzeru zonse.