64

Q.S Al-Anfal (8:64)

يٰٓاَيُّهَا النَّبِيُّ حَسْبُكَ اللّٰهُ وَمَنِ اتَّبَعَكَ مِنَ الْمُؤْمِنِيْنَ ࣖ

yā ayyuhan-nabiyyu ḥasbukallāhu wa manittaba‘aka minal-mu'minīn(a).

Iwe Mneneri (Muhammad)! Mulungu akukwanira (kukhala mtetezi) kwa iwe ndi kwa okhulupirira omwe akukutsatira.