38
Q.S Al-Anfal (8:38)
قُلْ لِّلَّذِيْنَ كَفَرُوْٓا اِنْ يَّنْتَهُوْا يُغْفَرْ لَهُمْ مَّا قَدْ سَلَفَۚ وَاِنْ يَّعُوْدُوْا فَقَدْ مَضَتْ سُنَّتُ الْاَوَّلِيْنَ
qul lil-lażīna kafarū in yantahū yugfar lahum mā qad salaf(a), wa iy ya‘ūdū faqad maḍat sunnatul-awwalīn(a).
Nena kwa osakhulupirira (Abu Sufyan ndi anzake kuti), "Ngati asiya (kusakhulupirira kwawo), Mulungu adzawakhululukira machimo awo akale; ndipo ngati abwereranso (kukamenyana ndi Mneneri) ndithudi, (kwa iwo) sunnah (ya Allah motsutsana) ndi akale (anawonongedwa) imagwira ntchito."