33

Q.S Al-Anfal (8:33)

وَمَا كَانَ اللّٰهُ لِيُعَذِّبَهُمْ وَاَنْتَ فِيْهِمْۚ وَمَا كَانَ اللّٰهُ مُعَذِّبَهُمْ وَهُمْ يَسْتَغْفِرُوْنَ

wa mā kānallāhu liyu‘ażżibahum wa anta fīhim, wa mā kānallāhu mu‘ażżibahum wa hum yastagfirūn(a).

Koma Mulungu sadzawalanga, bola ngati iwe (Muhammad) uli pakati pawo. Ndipo Mulungu sadzawalanganso, pamene iwo akadali kupempha chikhululukiro.