30
Q.S Al-Anfal (8:30)
وَاِذْ يَمْكُرُ بِكَ الَّذِيْنَ كَفَرُوْا لِيُثْبِتُوْكَ اَوْ يَقْتُلُوْكَ اَوْ يُخْرِجُوْكَۗ وَيَمْكُرُوْنَ وَيَمْكُرُ اللّٰهُ ۗوَاللّٰهُ خَيْرُ الْمٰكِرِيْنَ
wa iż yamkuru bikal-lażīna kafarū liyuṡbitūka au yaqtulūka au yukhrijūk(a), wa yamkurūna wa yamkurullāh(u), wallāhu khairul-mākirīn(a).
Ndipo (kumbukirani), pamene osakhulupirira (Aquraish) anaganiza zokuchitirani chiwembu (Muhammad) kuti akumangeni ndikukutsekerani m'ndende kapena kukuphani, kapena kukutulutsani, adapanga chinyengo ndipo Mulungu adaletsa chinyengocho. Mulungu ndiye wobwezera wabwino kwambiri wa chinyengo.