21

Q.S Al-Anfal (8:21)

وَلَا تَكُوْنُوْا كَالَّذِيْنَ قَالُوْا سَمِعْنَا وَهُمْ لَا يَسْمَعُوْنَۚ

wa lā takūnū kal-lażīna qālū sami‘nā wa hum lā yasma‘ūn(a).

Ndipo musakhale ngati (onyenga) amene amati, "Tamva," koma iwo samva (chifukwa mitima yawo ikukana).