17
Q.S Al-Anfal (8:17)
فَلَمْ تَقْتُلُوْهُمْ وَلٰكِنَّ اللّٰهَ قَتَلَهُمْۖ وَمَا رَمَيْتَ اِذْ رَمَيْتَ وَلٰكِنَّ اللّٰهَ رَمٰىۚ وَلِيُبْلِيَ الْمُؤْمِنِيْنَ مِنْهُ بَلَاۤءً حَسَنًاۗ اِنَّ اللّٰهَ سَمِيْعٌ عَلِيْمٌ
falam taqtulūhum wa lākinnallāha qatalahum, wa mā ramaita iż ramaita wa lākinallāha ramā, wa liyubliyal-mu'minīna minhu balā'an ḥasanā(n), innallāha samī‘un ‘alīm(un).
Kotero (kwenikweni) simunawaphe inu, koma Mulungu ndiye anawapha, ndipo simunawaphe pamene munaponya, koma Mulungu ndiye anaponya. (Mulungu anachita izi kuti awawononge) ndi kupatsa okhulupirira chigonjetso chabwino. Ndithudi, Mulungu ndi Wakumva Zonse, Wodziwa Zonse.