1

Q.S Al-Anfal (8:1)

يَسْـَٔلُوْنَكَ عَنِ الْاَنْفَالِۗ قُلِ الْاَنْفَالُ لِلّٰهِ وَالرَّسُوْلِۚ فَاتَّقُوا اللّٰهَ وَاَصْلِحُوْا ذَاتَ بَيْنِكُمْ ۖوَاَطِيْعُوا اللّٰهَ وَرَسُوْلَهٗٓ اِنْ كُنْتُمْ مُّؤْمِنِيْنَ

yas'alūnaka ‘anil-anfāl(i), qulil-anfālu lillāhi war-rasūl(i), fattaqullāha wa aṣliḥū żāta bainikum, wa aṭī‘ullāha wa rasūlahū in kuntum mu'minīn(a).

Akukufunsa (Muhammad) za (kugawa) zofunkha za nkhondo. Nena, "Zofunkha za nkhondo ndi za Allah ndi Mtumiki (monga mwa zomwe Allah ndi Mtumiki Wake amapereka), choncho opani Allah ndipo pangani ubale pakati pa anansi anu, ndipo mverani Allah ndi Mtumiki Wake ngati ndinu okhulupirira."