24

Q.S Al-Insan (76:24)

فَاصْبِرْ لِحُكْمِ رَبِّكَ وَلَا تُطِعْ مِنْهُمْ اٰثِمًا اَوْ كَفُوْرًاۚ

faṣbir liḥukmi rabbika wa lā tuṭi‘ minhum āṡiman au kafūrā(n).

Choncho pirira pa (kukwaniritsa) malamulo a Mbuye wako, ndipo usatsatire ochimwa ndi osakhulupirira pakati pawo.