10

Q.S Al-Insan (76:10)

اِنَّا نَخَافُ مِنْ رَّبِّنَا يَوْمًا عَبُوْسًا قَمْطَرِيْرًا

innā nakhāfu mir rabbinā yauman ‘abūsan qamṭarīrā(n).

Ndithudi, tikuopa (chilango cha) Mulungu tsiku limene anthu adzakhala ndi nkhope yowawa yodzaza ndi mavuto.”