6

Q.S Al-Muzzammil (73:6)

اِنَّ نَاشِئَةَ الَّيْلِ هِيَ اَشَدُّ وَطْـًٔا وَّاَقْوَمُ قِيْلًاۗ

inna nāsyi'atal-laili hiya asyaddu waṭ'aw wa aqwamu qīlā(n).

Zoonadi, kudzuka usiku kumakhala kolimba (kumadzaza moyo); ndipo (kuwerenga panthawiyo) kunali kochititsa chidwi kwambiri.