95

Q.S Al-A'raf (7:95)

ثُمَّ بَدَّلْنَا مَكَانَ السَّيِّئَةِ الْحَسَنَةَ حَتّٰى عَفَوْا وَّقَالُوْا قَدْ مَسَّ اٰبَاۤءَنَا الضَّرَّاۤءُ وَالسَّرَّاۤءُ فَاَخَذْنٰهُمْ بَغْتَةً وَّهُمْ لَا يَشْعُرُوْنَ

Ṡumma baddalnā makānas-sayyi'atil-ḥasanata ḥattā ‘afau wa qālū qad massa ābā'anaḍ-ḍarrā'u was-sarrā'u fa akhażnāhum bagtataw wa hum lā yasy‘urūn(a).

Kenako tidasintha mavuto ndi chisangalalo (kotero kuti ana awo ndi chuma chawo) zichuluke, kenako adati, "Ndithudi makolo athu adakumana ndi mavuto ndi chisangalalo," choncho tidawalanga mwadzidzidzi popanda iwo kuzindikira.