93

Q.S Al-A'raf (7:93)

فَتَوَلّٰى عَنْهُمْ وَقَالَ يٰقَوْمِ لَقَدْ اَبْلَغْتُكُمْ رِسٰلٰتِ رَبِّيْ وَنَصَحْتُ لَكُمْۚ فَكَيْفَ اٰسٰى عَلٰى قَوْمٍ كٰفِرِيْنَ ࣖ

fa tawallā ‘anhum wa qāla yā qaumi laqad ablagtukum risālāti rabbī wa naṣaḥtu lakum, fa kaifa āsā ‘alā qaumin kāfirīn(a).

Choncho Shuaib anawasiya nati, "E inu anthu anga! Ndithudi, ndakufikitsirani uthenga wa Mbuye wanga ndipo ndakulangizani. Ndiye ndingadandaule bwanji ndi osakhulupirira?"