90
Q.S Al-A'raf (7:90)
وَقَالَ الْمَلَاُ الَّذِيْنَ كَفَرُوْا مِنْ قَوْمِهٖ لَىِٕنِ اتَّبَعْتُمْ شُعَيْبًا اِنَّكُمْ اِذًا لَّخٰسِرُوْنَ
wa qālal-mala'ul-lażīna kafarū min qaumihī la'inittaba‘tum syu‘aiban innakum iżal lakhāsirūn(a).
Ndipo atsogoleri a anthu ake (Shuaib) omwe anali osakhulupirira anati (kwa wina ndi mnzake): "Ndithudi, ngati mutsatira Shuaib, ndithudi inu ndi omwe mudzatayika."