82
Q.S Al-A'raf (7:82)
وَمَا كَانَ جَوَابَ قَوْمِهٖٓ اِلَّآ اَنْ قَالُوْٓا اَخْرِجُوْهُمْ مِّنْ قَرْيَتِكُمْۚ اِنَّهُمْ اُنَاسٌ يَّتَطَهَّرُوْنَ
wa mā kāna jawāba qaumihī illā an qālū akhrijūhum min qaryatikum, innahum unāsuy yataṭahharūn(a).
Ndipo yankho la anthu ake silinali lina koma kunena kuti, "Atulutseni (Lut ndi otsatira ake) m'dziko lanu, ndi anthu omwe amadziona kuti ndi oyera."