73

Q.S Al-A'raf (7:73)

وَاِلٰى ثَمُوْدَ اَخَاهُمْ صٰلِحًاۘ قَالَ يٰقَوْمِ اعْبُدُوا اللّٰهَ مَا لَكُمْ مِّنْ اِلٰهٍ غَيْرُهٗۗ قَدْ جَاۤءَتْكُمْ بَيِّنَةٌ مِّنْ رَّبِّكُمْۗ هٰذِهٖ نَاقَةُ اللّٰهِ لَكُمْ اٰيَةً فَذَرُوْهَا تَأْكُلْ فِيْٓ اَرْضِ اللّٰهِ وَلَا تَمَسُّوْهَا بِسُوْۤءٍ فَيَأْخُذَكُمْ عَذَابٌ اَلِيْمٌ

wa ilā ṡamūda akhāhum ṣāliḥā(n), qāla yā qaumi‘budullāha mā lakum min ilāhin gairuh(ū), qad jā'atkum bayyinatum mir rabbikum, hāżihī nāqatullāhi lakum āyatan fa żarūhā ta'kul fī arḍillāhi wa lā tamassūhā bisū'in fa ya'khużakum ‘ażābun alīm(un).

Ndipo kwa anthu a Samud (Tidatumiza) m'bale wawo Saleh. Iye adati, "E inu anthu anga! Pembedzani Mulungu! Palibe mulungu wina koma Iye. Ndithudi, umboni womveka bwino wafika kwa inu kuchokera kwa Mbuye wanu. Ngamila iyi yaikazi yochokera kwa Mulungu ndi chizindikiro kwa inu. Iloleni idye panthaka ya Mulungu, musaiwononge, chifukwa chake mudzakhala ndi chilango chowawa."