64

Q.S Al-A'raf (7:64)

فَكَذَّبُوْهُ فَاَنْجَيْنٰهُ وَالَّذِيْنَ مَعَهٗ فِى الْفُلْكِ وَاَغْرَقْنَا الَّذِيْنَ كَذَّبُوْا بِاٰيٰتِنَاۗ اِنَّهُمْ كَانُوْا قَوْمًا عَمِيْنَ ࣖ

fa każżabūhu fa anjaināhu wal-lażīna ma‘ahū fil-fulki wa agraqnal-lażīna każżabū bi'āyātinā, innahum kānū qauman ‘amīn(a).

Choncho adamkana (Nowa). Kenako tidamupulumutsa iye ndi omwe anali naye m'chombo. Tidawamiza iwo amene akukana ma Aya athu. Ndithudi, iwo ndi anthu akhungu (maso a mitima yawo).