59
Q.S Al-A'raf (7:59)
لَقَدْ اَرْسَلْنَا نُوْحًا اِلٰى قَوْمِهٖ فَقَالَ يٰقَوْمِ اعْبُدُوا اللّٰهَ مَا لَكُمْ مِّنْ اِلٰهٍ غَيْرُهٗۗ اِنِّيْٓ اَخَافُ عَلَيْكُمْ عَذَابَ يَوْمٍ عَظِيْمٍ
laqad arsalnā nūḥan ilā qaumihī fa qāla yā qaumi‘budullāha mā lakum min ilāhin gairuh(ū), innī akhāfu ‘alaikum ‘ażāba yaumin ‘aẓīm(in).
Ndithudi, tidatumiza Nowa kwa anthu ake, kenako adati, "E inu anthu anga! Pembedzani Mulungu! Palibe mulungu wina kupatula Iye. Ndithudi, ndikuopa kuti mudzazunzidwa ndi chilango pa tsiku loopsa (lachimaliziro).