5

Q.S Al-A'raf (7:5)

فَمَا كَانَ دَعْوٰىهُمْ اِذْ جَاۤءَهُمْ بَأْسُنَآ اِلَّآ اَنْ قَالُوْٓا اِنَّا كُنَّا ظٰلِمِيْنَ

famā kāna da‘wāhum iż jā'ahum ba'sunā illā an qālū innā kunnā ẓālimīn(a).

Choncho chilango chathu chitafika pa iwo, madandaulo awo sanali ena koma kunena kuti, "Ndithudi, ife tinali ochita zoipa."