46

Q.S Al-A'raf (7:46)

وَبَيْنَهُمَا حِجَابٌۚ وَعَلَى الْاَعْرَافِ رِجَالٌ يَّعْرِفُوْنَ كُلًّا ۢ بِسِيْمٰىهُمْۚ وَنَادَوْا اَصْحٰبَ الْجَنَّةِ اَنْ سَلٰمٌ عَلَيْكُمْۗ لَمْ يَدْخُلُوْهَا وَهُمْ يَطْمَعُوْنَ

wa bainahumā ḥijāb(un), wa ‘alal-a‘rāfi rijāluy ya‘rifūna kullam bisīmāhum, wa nādau aṣḥābal-jannati an salāmun ‘alaikum, lam yadkhulūhā wa hum yaṭma‘ūn(a).

Ndipo pakati pawo (anthu okhala ku Paradaiso ndi ku Gehena) pali chophimba, ndipo pa A'raf (malo okwezeka kwambiri) pali anthu ozindikirana, aliyense ndi zizindikiro zake. Adzaitana anthu okhala ku Paradaiso kuti, "Mtendere ukhale pa inu." Iwo sanalowebe, koma akufunitsitsa (kulowa).