34

Q.S Al-A'raf (7:34)

وَلِكُلِّ اُمَّةٍ اَجَلٌۚ فَاِذَا جَاۤءَ اَجَلُهُمْ لَا يَسْتَأْخِرُوْنَ سَاعَةً وَّلَا يَسْتَقْدِمُوْنَ

wa likulli ummatin ajal(un), fa iżā jā'a ajaluhum lā yasta'khirūna sā‘ataw wa lā yastaqdimūn(a).

Ndipo anthu onse ali ndi nthawi yawo ya imfa (nthawi yoikika). Imfa yawo ikafika, sangapemphe kuchedwa kapena kufulumizitsidwa kwa kanthawi.