31

Q.S Al-A'raf (7:31)

۞ يٰبَنِيْٓ اٰدَمَ خُذُوْا زِيْنَتَكُمْ عِنْدَ كُلِّ مَسْجِدٍ وَّكُلُوْا وَاشْرَبُوْا وَلَا تُسْرِفُوْاۚ اِنَّهٗ لَا يُحِبُّ الْمُسْرِفِيْنَ ࣖ

yā banī ādama khużū zīnatakum ‘inda kulli masjidiw wa kulū wasyrabū wa lā tusrifū, innahū lā yuḥibbul-musrifīn(a).

Inu ana a Adamu! Valani zovala zanu zabwino nthawi iliyonse mukalowa mu mzikiti, idyani ndi kumwa, koma musapitirire. Ndithudi, Mulungu sakonda anthu ochulukitsa.