26

Q.S Al-A'raf (7:26)

يٰبَنِيْٓ اٰدَمَ قَدْ اَنْزَلْنَا عَلَيْكُمْ لِبَاسًا يُّوَارِيْ سَوْءٰتِكُمْ وَرِيْشًاۗ وَلِبَاسُ التَّقْوٰى ذٰلِكَ خَيْرٌۗ ذٰلِكَ مِنْ اٰيٰتِ اللّٰهِ لَعَلَّهُمْ يَذَّكَّرُوْنَ

yā banī ādama qad anzalnā ‘alaikum libāsay yuwārī sau'ātikum wa rīsyā(n), wa libāsut-taqwā żālika khair(un), żālika min āyātillāhi la‘allahum yażżakkarūn(a).

Inu ana a Adamu! Ndithudi, takupatsani zovala zophimba umaliseche wanu ndi zokongoletsera zanu. Koma zovala za kuopa Mulungu, zimenezo ndi zabwino kwambiri. Izi ndi zina mwa zizindikiro za mphamvu ya Mulungu, tikukhulupirira kuti adzazikumbukira.