23

Q.S Al-A'raf (7:23)

قَالَا رَبَّنَا ظَلَمْنَآ اَنْفُسَنَا وَاِنْ لَّمْ تَغْفِرْ لَنَا وَتَرْحَمْنَا لَنَكُوْنَنَّ مِنَ الْخٰسِرِيْنَ

qālā rabbanā ẓalamnā anfusanā wa illam tagfir lanā wa tarḥamnā lanakūnanna minal-khāsirīn(a).

Onse awiri anati, "Mbuye wathu, tadzichitira tokha zoipa. Ngati simutikhululukira ndi kutichitira chifundo, ndithudi tidzakhala m'gulu la otaika."