200
Q.S Al-A'raf (7:200)
وَاِمَّا يَنْزَغَنَّكَ مِنَ الشَّيْطٰنِ نَزْغٌ فَاسْتَعِذْ بِاللّٰهِ ۗاِنَّهٗ سَمِيْعٌ عَلِيْمٌ
wa immā yanzagannaka minasy-syaiṭāni nazgun fasta‘iż billāh(i), innahū samī‘un ‘alīm(un).
Ndipo ngati Satana abwera kudzakuyesani, dzitetezeni kwa Mulungu, ndithudi, Iye ndi Wakumva Zonse, Wodziwa Zonse.