193
Q.S Al-A'raf (7:193)
وَاِنْ تَدْعُوْهُمْ اِلَى الْهُدٰى لَا يَتَّبِعُوْكُمْۗ سَوَۤاءٌ عَلَيْكُمْ اَدَعَوْتُمُوْهُمْ اَمْ اَنْتُمْ صٰمِتُوْنَ
wa in tad‘ūhum ilal-hudā lā yattabi‘ūkum, sawā'un ‘alaikum ada‘autumūhum am antum ṣāmitūn(a).
Ndipo ngati inu (Inu opembedza mafano) mutawaitana (mafano) kuti akutsogolereni, mafanowo sadzatha kulandira kuitana kwanu; ndi chimodzimodzi (zotsatira) kaya mutawaitana kapena kukhala chete.