191
Q.S Al-A'raf (7:191)
اَيُشْرِكُوْنَ مَا لَا يَخْلُقُ شَيْـًٔا وَّهُمْ يُخْلَقُوْنَۖ
ayusyrikūna mā lā yakhluqu syai'aw wa hum yukhlaqūn(a).
N’chifukwa chiyani akumuphatikiza (Allah) ndi chinthu (fano) chomwe sichingalenge chilichonse? Ngakhale kuti (mafano) okha ndi omwe adalengedwa.