Q.S Al-A'raf (7:189)
۞ هُوَ الَّذِيْ خَلَقَكُمْ مِّنْ نَّفْسٍ وَّاحِدَةٍ وَّجَعَلَ مِنْهَا زَوْجَهَا لِيَسْكُنَ اِلَيْهَاۚ فَلَمَّا تَغَشّٰىهَا حَمَلَتْ حَمْلًا خَفِيْفًا فَمَرَّتْ بِهٖ ۚفَلَمَّآ اَثْقَلَتْ دَّعَوَا اللّٰهَ رَبَّهُمَا لَىِٕنْ اٰتَيْتَنَا صَالِحًا لَّنَكُوْنَنَّ مِنَ الشّٰكِرِيْنَ
huwal-lażī khalaqakum min nafsiw wāḥidatiw waja‘ala minhā zaujahā liyaskuna ilaihā, falammā tagasysyāhā ḥamalat ḥamlan khafīfan fa marrat bih(ī), falammā aṡqalad da‘awallāha rabbahumā la'in ātaitanā ṣāliḥan lanakūnanna minasy-syākirīn(a).
Iye ndiye amene anakulengani kuchokera mu mzimu umodzi (Adamu) ndipo kuchokera mmenemo analenga mkazi wake, kuti akondwere naye. Choncho atasakaniza, (mkazi wake) anatenga pakati pa mimba yopepuka, ndipo mkaziyo anapitiriza kumva yopepuka (kwa kanthawi). Kenako atamva kulemedwa, onse awiri (mwamuna ndi mkazi) anapempha Allah, Mbuye wawo (nati), "Ngati Mutipatsa mwana wolungama, ndithudi tidzakhala oyamikira nthawi zonse."