171
Q.S Al-A'raf (7:171)
۞ وَاِذْ نَتَقْنَا الْجَبَلَ فَوْقَهُمْ كَاَنَّهٗ ظُلَّةٌ وَّظَنُّوْٓا اَنَّهٗ وَاقِعٌۢ بِهِمْۚ خُذُوْا مَآ اٰتَيْنٰكُمْ بِقُوَّةٍ وَّاذْكُرُوْا مَا فِيْهِ لَعَلَّكُمْ تَتَّقُوْنَ ࣖ
wa iż nataqnal-jabala fauqahum ka'annahum ẓullatuw wa ẓannū annahū wāqi‘um bihim, khużū mā ātainākum biquwwatiw ważkurū mā fīhi la‘allakum tattaqūn(a).
Ndipo (kumbukirani) pamene tidakweza phiri pamwamba pawo, zinali ngati kuti (phirilo) laphimbidwa ndi mtambo ndipo anali otsimikiza kuti (phirilo) lidzawagwera. (Ndipo tidawauza kuti), "Gwirani mwamphamvu zomwe takupatsani, ndipo nthawi zonse kumbukirani (chitani) zomwe zili mmenemo kuti mukhale anthu oopa Mulungu."