Q.S Al-A'raf (7:158)
قُلْ يٰٓاَيُّهَا النَّاسُ اِنِّيْ رَسُوْلُ اللّٰهِ اِلَيْكُمْ جَمِيْعًا ۨالَّذِيْ لَهٗ مُلْكُ السَّمٰوٰتِ وَالْاَرْضِۚ لَآ اِلٰهَ اِلَّا هُوَ يُحْيٖ وَيُمِيْتُۖ فَاٰمِنُوْا بِاللّٰهِ وَرَسُوْلِهِ النَّبِيِّ الْاُمِّيِّ الَّذِيْ يُؤْمِنُ بِاللّٰهِ وَكَلِمٰتِهٖ وَاتَّبِعُوْهُ لَعَلَّكُمْ تَهْتَدُوْنَ
qul yā ayyuhan-nāsu innī rasūlullāhi ilaikum jamī‘anil-lażī lahū mulkus-samāwāti wal-arḍ(i), lā ilāha illā huwa yuḥyī wa yumīt(u), fa āminū billāhi wa rasūlihin-nabiyyil-ummiyyil-lażī yu'minu billāhi wa kalimatihī wattabi‘ūhu la‘allakum tahtadūn(a).
Nenani (Muhammad), "Inu anthu! Ndithudi, ine ndine Mtumiki wa Allah kwa inu nonse, Amene ali ndi ufumu wa kumwamba ndi dziko lapansi; palibe mulungu (yemwe ali ndi ufulu wopembedzedwa) koma Iye yekha, Amene amapereka moyo ndi imfa, kotero mukhulupirire Allah ndi Mtumiki Wake, (yemwe ndi) Mneneri wa Ummi amene amakhulupirira Allah ndi mawu Ake (mabuku Ake). Mutsateni, kuti muwongoleredwe."