155

Q.S Al-A'raf (7:155)

وَاخْتَارَ مُوْسٰى قَوْمَهٗ سَبْعِيْنَ رَجُلًا لِّمِيْقَاتِنَا ۚفَلَمَّآ اَخَذَتْهُمُ الرَّجْفَةُ قَالَ رَبِّ لَوْ شِئْتَ اَهْلَكْتَهُمْ مِّنْ قَبْلُ وَاِيَّايَۗ اَتُهْلِكُنَا بِمَا فَعَلَ السُّفَهَاۤءُ مِنَّاۚ اِنْ هِيَ اِلَّا فِتْنَتُكَۗ تُضِلُّ بِهَا مَنْ تَشَاۤءُ وَتَهْدِيْ مَنْ تَشَاۤءُۗ اَنْتَ وَلِيُّنَا فَاغْفِرْ لَنَا وَارْحَمْنَا وَاَنْتَ خَيْرُ الْغٰفِرِيْنَ

wakhtāra mūsā qaumahū sab‘īna rajulal limīqātinā, falammā akhażathumur-rajfatu qāla rabbi lau syi'ta ahlaktahum min qablu wa iyyāy(a), atuhlikunā bimā fa‘alas-sufahā'u minnā, in hiya illā fitnatuk(a), tuḍillu bihā man tasyā'u wa tahdī man tasyā'(u), anta waliyyunā fagfir lanā warḥamnā wa anta khairul-gāfirīn(a).

Ndipo Mose anasankha anthu makumi asanu ndi awiri mwa anthu ake kuti (atipemphe kulapa) pa nthawi imene tidakonza. Pamene adagwidwa ndi chivomerezi, Mose anati, "Mbuye wanga, mukadafuna, mukadawaononga iwo ndi ine tisanachite izi. Kodi mungationonge chifukwa cha zochita za anthu osazindikira pakati pathu? Zimenezo ndi mayeso ochokera kwa Inu, Mumasokeretsa ndi mayeso awa amene Mukufuna ndipo Mumatsogolera amene Mukufuna. Inu ndinu mtsogoleri wathu, choncho tikhululukireni ndi kutipatsa chifundo. Inu ndinu wokhululukira kwambiri."