149
Q.S Al-A'raf (7:149)
وَلَمَّا سُقِطَ فِيْٓ اَيْدِيْهِمْ وَرَاَوْا اَنَّهُمْ قَدْ ضَلُّوْاۙ قَالُوْا لَىِٕنْ لَّمْ يَرْحَمْنَا رَبُّنَا وَيَغْفِرْ لَنَا لَنَكُوْنَنَّ مِنَ الْخٰسِرِيْنَ
wa lammā suqiṭa fī aidīhim wa ra'au annahum qad ḍallū, qālū la'il lam yarḥamnā rabbunā wa yagfir lanā lanakūnanna minal-khāsirīn(a).
Ndipo pamene adanong'oneza bondo pa zochita zawo ndi kuzindikira kuti asochera, adati, "Ngati Ambuye wathu satichitira chifundo ndi kutikhululukira, tidzakhala m'gulu la otaika."