146

Q.S Al-A'raf (7:146)

سَاَصْرِفُ عَنْ اٰيٰتِيَ الَّذِيْنَ يَتَكَبَّرُوْنَ فِى الْاَرْضِ بِغَيْرِ الْحَقِّۗ وَاِنْ يَّرَوْا كُلَّ اٰيَةٍ لَّا يُؤْمِنُوْا بِهَاۚ وَاِنْ يَّرَوْا سَبِيْلَ الرُّشْدِ لَا يَتَّخِذُوْهُ سَبِيْلًاۚ وَاِنْ يَّرَوْا سَبِيْلَ الْغَيِّ يَتَّخِذُوْهُ سَبِيْلًاۗ ذٰلِكَ بِاَنَّهُمْ كَذَّبُوْا بِاٰيٰتِنَا وَكَانُوْا عَنْهَا غٰفِلِيْنَ

sa'aṣrifu ‘an āyātiyal-lażīna yatakabbarūna fil-arḍi bigairil-ḥaqq(i), wa iy yarau kulla āyatil lā yu'minū bihā, wa iy yarau sabīlar-rusydi lā yattakhiżūhu sabīlā(n), wa iy yarau sabīlal-gayyi yattakhiżūhu sabīlā(n), żālika bi'annahum każżabū bi'āyātinā wa kānū ‘anhā gāfilīn(a).

Ndidzachotsa zizindikiro (za mphamvu Zanga) kwa iwo amene amadzitamandira padziko lapansi popanda chifukwa chomveka. Ngakhale ataona chizindikiro chilichonse (cha mphamvu Zanga) sakanachikhulupirira. Ndipo ngati ataona njira yopita ku chitsogozo, sadzaitsatira, koma ngati ataona njira yolakwika, amaitsatira. Izi zili choncho chifukwa chakuti akukana zizindikiro Zathu ndipo nthawi zonse sazisamala.