144

Q.S Al-A'raf (7:144)

قَالَ يٰمُوْسٰٓى اِنِّى اصْطَفَيْتُكَ عَلَى النَّاسِ بِرِسٰلٰتِيْ وَبِكَلَامِيْ ۖفَخُذْ مَآ اٰتَيْتُكَ وَكُنْ مِّنَ الشّٰكِرِيْنَ

qāla yā mūsā inniṣṭafaituka ‘alan-nāsi birisālātī wa bikalāmī, fa khuż mā ātaituka wa kum minasy-syākirīn(a).

(Mulungu) anati, "E iwe Musa! Ndithudi, ine ndakusankhira (ndikusankha) pakati pa anthu ena (m'nthawi yako) kuti unyamule uthenga wanga ndi mawu anga, choncho gwira mwamphamvu zomwe ndakupatsani ndipo ukhale m'gulu la oyamikira."