134
Q.S Al-A'raf (7:134)
وَلَمَّا وَقَعَ عَلَيْهِمُ الرِّجْزُ قَالُوْا يٰمُوْسَى ادْعُ لَنَا رَبَّكَ بِمَا عَهِدَ عِنْدَكَۚ لَىِٕنْ كَشَفْتَ عَنَّا الرِّجْزَ لَنُؤْمِنَنَّ لَكَ وَلَنُرْسِلَنَّ مَعَكَ بَنِيْٓ اِسْرَاۤءِيْلَ ۚ
wa lammā waqa‘a ‘alihimur-rijzu qālū yā mūsad‘u lanā rabbaka bimā ‘ahida ‘indak(a), la'in kasyafta ‘annar-rijza lanu'minanna laka wa lanursilanna ma‘aka banī isrā'īl(a).
Ndipo pamene adakumana ndi chilango (chomwe chafotokozedwa) adati, "E, Musa! Tipemphe kwa Mbuye wako monga momwe adakulonjezera. Ngati ungatichotsere chilango ichi, tidzakukhulupirira ndipo tidzalola ana a Israeli kupita nawe."